
kell kay - sunandi كلمات أغنية
[intro]
exclusive
namva ukuwuza anzako ndimakukamira
umandikamba ku mbali k_mati vinyo adatha
ndikakutsamila pa chifuwa, mavantha ndikuwawasa
you can’t do this anymore, kuthetsa mpaka mu chizungu
y’all ready know
[chorus]
i hope you remember
you said you would be my defender
zalowa ma temper
i miss our time together
sunandi sunandiwuze bwanji?
kuti uzandi uzandisiya chonchi?
sunandi sunandiwuze bwanji?
kuti focus, focus ili pa ena?
[verse 1]
lonse inali bodza, zikundivuta k_mvetsa
what went wrong my darling? i’m sorry i [?] my darling
nd_nkachimwa cholinga iwe upulimuke
ndikalakwitsa cholinga iweyo usadabwe
nd_nkakonza njira kuti iweyo usatelereke
nd_nkawona ngati uphunzira
koma unaphunzira kukonda wena
[chorus]
i hope you remember
you said you would be my defender
zalowa ma tempеr
i miss our time together
sunandi sunandiwuzе bwanji?
kuti uzandi uzandisiya chonchi?
sunandi sunandiwuze bwanji?
kuti focus, focus ili pa ena?
[verse 2]
because i know sindisisita[?]
kufuna zowopa zathu darling
tell me what you loved?
and what brought you to tears?
i opened up my heart and i shared all my flaws
but you never said a word
kuti uzandisiya pa mpepho
to the moments we’ll never share
experience we’ll never have
laughter we’ll never rejoy
moments that slipped away
a future we will never have to get through
dreams that never came to be
wandilakwira darling
ndikakonza njira kuti iweyo usateleke
nd_nkati uphunzira
koma uphunzira kukonda wena
[chorus]
i hope you remember (i hope you remember)
you used to be my (you said you would be my defender)
zalowa ma temper (zalowa ma temper)
i missed you darling (i miss our times together)
[bridge]
after everything there is someone
kodi tinali chabe mistake?
how did we go from talking every minute?
to not talking at all
ndimalephela chani? ndi patipo sindimafikira?
zoti ndinali perfect, unkandinamiza?
[chorus]
i hope you remember (oh darling)
you said you would be my defender
zalowa (zalowa ma temper)
i miss our time together (i miss our time together)
(sunandi) sunandi sunandiwuze bwanji?
kuti uzandi uzandisiya chonchi?
(sunandi) sunandi sunandiwuze bwanji?
kuti focus, focus ili pa ena?
كلمات أغنية عشوائية
- charley patton - tom rushen blues كلمات أغنية
- dani faiv - s.w.n.c. كلمات أغنية
- casualsexclub - consume كلمات أغنية
- afrob (deu) - zeit كلمات أغنية
- jimmy fortune - i believe كلمات أغنية
- far east movement - daymitfeelsgood كلمات أغنية
- curtis striker - mf nigga كلمات أغنية
- gunplay - bible on the dash pt. 2 كلمات أغنية
- andreas bourani - wunder - ltm remix كلمات أغنية
- liber & sylwia grzeszczak - co z nami będzie كلمات أغنية