kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kell kay - loss كلمات الأغنية

Loading...

(kuluza ineyo eti)
(waluza makina eti)
(kuluza zonsezi eti)

ona makani, chibwana
waluza nazo, makina
i’m tired of stressing over silly things
bola nkapeze zina

i’m done with your love
i’m done with your love
i’m giving my love to another
i’m giving my love

in my life
i regret the love i
gave to you my time, now
n’kampatsa another

’cause in my life
i regret the love i
gave to you my time, now
n’kampatsa another

iwe, kuluza ine
kusiya ine
wataya makina
your loss
iwe, kuluza ine
kusiya ine
wataya makina
your loss

your loss, (kuluza ineyo eti)
your loss
your loss, (kutaya inеyo eti)
your loss, (wataya makina eti)

that’s your loss

nd_nkamanga nyumba yathu ona foundation
ma regrеt
nd_nkapanga plan boat waku vacation
ma regret
nd_nkafuna banja lathu lizanke kenani
ma regret
your loss your loss unataya mamuna wa vision
ma regret

cause in my life
i regret the love i
gave to you my time
now, n’kampatsa another
cause in my life
i regret the love i
gave to you my time
now, n’kampatsa another

iwe, kuluza ine
kusiya ine
wataya makina
your loss

iwe, kuluza ine
kusiya ine
wataya makina
your loss

your loss, (kuluza ineyo eti)
your loss
your loss, (kutaya ineyo eti)
your loss, (wataya makina eti)

that’s your loss (your loss)

in my life
i regret the love i
gave to you my time, now
n’kampatsa another
vuto lomazimva mwafikapo
koma nane ma option ndilinawo angapo
vuto lomvera anzako
uone m’mene atandandire ukachoka
chimaphweka chikakhala chako
ena kusalira kudya
ma dosage aku mlakho
mmene umandisiya wati ndiona zilango
osayenera mfumu ndiwe mfana opanda mwambo
siukonda mzako mmene uzikondera mwini
mwina chitauni, umazimva ukaswiri
ndisaname mamie you were my achilles
wataya machina osadetsedwa ndi dzimbiri
time will tell wasewera game yoluza
karma ikuk_maliza ndimfana ozunza
play this on repeat wherever you are
mtima wamunthu siosewera nawo juga

iwe unkanyada
nd_nkangok_mvera zinkhani
unkandisungira kampeni
siunkamva anga ma plan
nnakuuza over and over
and you ever tell me that its over
nzako ujanso ndi njoka
wataya nazo chi joker

’cause in my life
i regret the love i
gave to you my time
now, n’kampatsa another

’cause in my life
i regret the love i
gave to you my time
now, n’kampatsa another

iwe, kuluza ine
kusiya ine
wataya makina
your loss

iwe, kuluza ine
kusiya ine
wataya makina
your loss

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...