kamarih - zidutswa كلمات الأغنية
mmh mmh mmh mmh mmh
come on yeah
i heard all about you
koma nd_nkayesa uzasintha ndi chikondi yeah
i just couldn’t face the truth
i chose to be blinded by your body
abale atandiletsa sind’amvere nd_nkayesa angopanga chabe nsanje
oh nsanje angopanga chabe nsanje
anzanga atandiletsa sind’amvere nd_nkayesa angofuna andilande
ah ndilande nd_nkayesa andilanda
pano w_ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw_nga
zidutswa m’mtima mw_nga
w_ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw_nga
waswa mtima w_nga yeah
no one left here to lean on
no one there to save me i’m going under
i chose you above it all
pano ndaphula zibwana zanga
abale atandiletsa sind’amvere nd_nkayesa angopanga chabe nsanje
oh nsanje angopanga chabe nsanje
anzanga atandiletsa sind’amvere nd_nkayesa angofuna andilande
ah ndilande nd_nkayesa andilanda
pano w_ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw_nga
zidutswa m’mtima mw_nga
w_ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw_nga
waswa mtima w_nga yeah
كلمات أغنية عشوائية
- rancho y barrio - el h-1 “conejo” كلمات الأغنية
- loski - avengers كلمات الأغنية
- ana bulnes - roatán كلمات الأغنية
- moses. and breeze - four walls كلمات الأغنية
- p.konrad - furgonetka كلمات الأغنية
- jeremiah paltan - sweet melodies كلمات الأغنية
- david luján shedda - seis letras كلمات الأغنية
- perfectly damaged - american dream كلمات الأغنية
- don hidalgo - a letter 4 u كلمات الأغنية
- healer (usa) - alpha كلمات الأغنية