kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

k2b block - kulinka ndi abale كلمات أغنية

Loading...

[chorus: crispy malawi]
kd_z made da beat
chaku kawale ndungolinker ndi abale
party after party utha kuyesa za ndale
komwe kwayaka motoko sitingakhale
sitingadane ndungofuna n_n_le
life imasintha ground
tawona tinasintha sound
tawona tinapanga noun
tili ndi ma home, tili ndima hoes, tili ndima homies

[verse 1: blaq kid]
wona patali kuyiwerenga ngati mawu
kuyimba za nchito fanzi ikungoti wow
from k1 to k2, ndak_mana ndi achina keturah
atatchena akulowela ku institute
ndiwanyamule mu suzuki swift
light up a leaf let me take a spliff
puff, puff

[verse 2: kd_z]
kd_z baby
ndili mu hood (hood)
hats off when you see us ndife mafumu
any moods
sipazakhala kd_z wina ndine modzi
one and only
[verse 3: georj_z & crispy malawi ]
lero ndikugawa ma moni (ma moni)
moni ndi ulele sufunika makobidi
osayakha ndimchapa ma kofi
maso afila (yeah, yeah) maso afila (yeah, yeah)

[chorus: crispy malawi]
chaku kawale ndungolinker ndi abale
party after party utha kuyesa za ndale
komwe kwayaka motoko sitingakhale
sitingadane ndungofuna n_n_le ha
life imasintha ground
tawona tinasintha sound
tawona tinapanga noun
tili ndi ma home, tili ndima hoes, tili ndima homies

[verse 3: dirty flo]
ndinali konko nane
kuyiphula kwake kopanda mbale
malo ndi ambiri tisakankhane
game ndinagoylowa ngati ndine sunset
undizungilre pachi corner
umagwira kuti? sindimakuona
uziwe ndine performer
water, water ndine toner
munali kuti malinga sindingakugwirere nchito
mphevu yake yodyera munthiko
[verse 4: krazie g]
im in your city i’m your hood tidyetse ndudu
the girls look pretty they look like fupa lolowa msuzi
i’m feelin witty with my g’s
hate rats love cheese
ndili pa easy ku runner st__z
palibe ompanga please, apa ben 10 avine
ndik_mpatsa keke ndine, ndili ndi gang, gang inde
ndife ma tycoon ku chilinde
ndine style bender ima ndipinde, ndipinde, nde, nde
ma babe aku twerker, sound ikublaster
ife tangosweka timacheza ndima zaza
kudabwa ndikuseka ndine wokwiya aku judger
ndine case tangocheker dzulo so ndangona panja
street n_gga g wamisala
ndiku charger 8 figures, wolipira wabisala
i’ve been getting bigger mpaka ndamva kwa sarah
akuti bwanji ukundisala kundisala?

[chorus: crispy malawi]
chaku kawale ndungolinker ndi abale
party after party utha kuyesa za ndale
komwe kwayaka motoko sitingakhale
sitingadane ndungofuna n_n_le
life imasintha ground
tawona tinasintha sound
tawona tinapanga noun
tili ndi ma home, tili ndima hoes, tili ndima homies
[verse 6: adah yung_z]
tili mudzi ku chiller ndi achina pwethu
anthu azunguza oduka mitu achina nkhwezu
sitimawopa kuyenda usiku ngati nkhwezula
mphini zinayenda nde munthu sangati chesule (chesule)
basi ife tungochiller ndima homies
muyimile mkazi uyu umenye h_rn (h_rn)
pipipipi! menya h_rn (h_rn)
andipatsa number yake mpatse phone
(lamya)

[verse 7: georjiz]
ndadzuka m’mawa kuyima pa people’s
funa mupeze chilembwe or lincoln
daily benjamin’s
wandihalla ringtone
iwe ndi matsile basi opanda chi winter
halla to my n_gga wash halla to me
halla to my hustle ndimadya nthuli (diba doba)
ndili ndi a heavy sungalamulire
halla k2b, halla ifeyo

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغنية الشائعة حالياً

Loading...