kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

jeg tellem - bona كلمات الأغنية

Loading...

yahman yah

tellem

zomwe ndik_maona

dziko li linagona

satana pano anangolowa paliponse kulimeza ngati chi ng’ona

akufalitsa ti mabodza

angofuna kuti pomboneza

eti uthenga wabho ena ati ndizanyasi mhhu muk_manyoza ah ah

koma sindingasiye ku praiser ine praiser ine eh

ndimamutsata yahweh ndipo ndimamupembeza ine mbeza ine hey

masten aziziwa mawu awo mawasungabe sungabe eh

uzikonda chauta
namalenga pokusunga iwe sunga iwe hey

devil yo k_mubona ahah

mpaka ak_magoma ahah

wak_mana ndi chiphona ah

sundikopa kopa ase

devil yo k_mubona mmhu

mpaka ak_magoma mmhu

wak_mana ndi chiphona

sundikopa kopa ase

ey yeah yah

ndipo sinkuopa ase

ey yeeh yah

sundikopa kopa ase
ey yeah yah

ndipo sinkuopa ase

ey yeah yah

kuyimba nako kukayamba kukoma

satana naye nde saku mapuma

akusaka tinjira atikole tizimupopa koma wagoma

nyengo zaka nazo zikayamba kusintha

ndipamene akufuna ndizifuntha

kenako nkhale desperate ndimutsate eti sindipanga izi ataaa

koma sindingasiye ku praiser ine praiser ine eh

ndimamutsata yahweh ndipo ndimamupembeza ine mbeza ine hey

masten aziziwa mawu awo mawasungabe sungabe eh
uzikonda chauta

namalenga pokusunga iwe sunga iwe hey

devil yo k_mubona ah ah

mpaka ak_magoma ah ah

wak_mana ndi chiphona ah

sundikopa kopa ase

devil yo k_mubona mmhu

mpaka ak_magoma mmhuu

wak_mana ndi chiphona

sundikopa kopa ase

ey yeay yah

ndipo sinkuopa ase

ey yeah yah

sundikopa kopa ase

ey yeah yah

ndipo sinkuopa ase

ey yeah yah

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...