kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

james chirwa - kumapanga za ine كلمات الأغنية

Loading...

(pre_hook)
mta!
lingalira
mmene k_mwambaku
k_machitira (nthawi zonse!)

olo nsanasithe njira
ndipo kwakhala
kukundichengetera (eti inu!)

ndipo sik_masiya k_machitabe
chimodzimodzi (indee!)

kunkapanga, kukupanga
k_mapanga za ine

(hook)
k_mapanga za ndani?
za ine
k_mapanga za nda?
za ine
k_mapanga za ndani?
za awo, za iwe, za ine

k_mapanga za ndani?
za ine
k_mapanga za nda?
za ine
k_mapanga za ndani?
za awo, za iwe, za ine
[verse 1]

that’s why
can’t let myself to fall
in the lake of fear
for my master & father
is always with me here

for we was born in sin
so he gave his only son
it wasn’t for show off but
for us a perfect plan

nde sawodzera
sagona
sizimphonya zonse amaona
khutu lake silogontha
nthawi zonse avetsera
ndipo amamva
iye ndiye m’busa w_nga
andiyang’anila konse ndiyenda
alinane konse ndiyenda
ndilibe mantha…

“in the bible
‘exodus 14 v 14’
the bible says the lord will fight for you and all you have to do is to keep still ”
(pre_hook)
mta!
lingalira
mmene k_mwambaku
k_machitira (nthawi zonse!)

olo nsanasithe njira
ndipo kwakhala
kukundichengetera (eti inu!)

ndipo sik_masiya k_machitabe
chimodzimodzi (indee!)

kunkapanga, kukupanga
k_mapanga za ine

(hook)
k_mapanga za ndani?
za ine
k_mapanga za nda?
za ine
k_mapanga za ndani?
za awo, za iwe, za ine

k_mapanga za ndani?
za ine
k_mapanga za nda?
za ine
k_mapanga za ndani?
za awo, za iwe, za ine
[verse 2]

mtendere okha okha
ndipo siwa pokha pokha
sandisiya ndekha ndekha
amenya nkhondo mtangodekha

nthawi iliyonse
ali okozeka utha
kuyenda naye (kuyenda naye)
unaganiza bho ngati unasakha
kuyenda naye (kuyenda naye)

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...