
isaac liwotcha - musalire كلمات أغنية
“[verse]
ndidaona (zodabwitsa)
panthawi (yamavuto) oh mama
akuchikazi (adatenga)
katundu yense (ndi ana omwe) oh mama
bambo awo (akali moyo)
koma ana onse (adawalanda) oh mama
ana asowadi (chikondi)
akhalangati (akapolo) oh mama
“[verse]
mukadatenga (katundu yekha)
sichikanakhala (chovuta) oh mama
koma mwatenga (ndi ana omwe)
kuwaika mgulu (lakatundu) oh mama
ana w_nga ndithu (akuvutika)
pamene ine (ndilipo) oh mama
nthawi zonse (ndimangolira)
kulilira (ana w_nga) oh mama
“[chorus]
ana anga musalire
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
ana anga musalire
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
“[verse]
mbuye mverani (kulira kw_nga)
magazi anga (akuvutika) oh mama
mtima w_nga (umafuna)
nditamakhala (ndi ana w_nga) oh mama
koma poti (adandilanda)
ana w_nga (amangolira) oh mama
abambo wathu (ali kuti?)
inu agogo (mutipelekeze) oh mama
“[verse]
ana anga (mudzipemphera)
ambuye amamva (mapemphero) oh mama
musade nkhawa (ambuye alipo)
ndiye adziku (tetezani) oh mama
nthawi zonse (mukamalira)
mtima mw_nga (chisoni) oh mama
ndipempha mbuye (namalenga)
kuti aku (yang’aneni) oh mama
“[chorus]
ana anga musalirе
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
ana anga musalirе
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
كلمات أغنية عشوائية
- aino venna - marlene كلمات أغنية
- ibo k payne - miente luna كلمات أغنية
- allen wadlo williams - moonbow كلمات أغنية
- crooked i - big dreams كلمات أغنية
- crooked i - black pussy كلمات أغنية
- jenn bostic - gay or taken كلمات أغنية
- cherieo nakednoiz - frustrated كلمات أغنية
- gloria gaynor - o holy night كلمات أغنية
- e 40 - chitty bang كلمات أغنية
- crooked i - dream big كلمات أغنية