gwamba - akondakitale كلمات أغنية
[intro: lawi]
yi, aye_iye_yah
aye_iye_yah
[chorus: lawi]
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje

ulendo w_nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w_nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 1:gwamba]
aish, ndalama nde yavuta pa nyasa
daily fans k_mayisaka
sikuwona zoti ndiwe shasha
k_menya business basi k_mayitsatsa
nde mukapeza ka ndalama sister, chonde k_makagwiritsitsa
mukamagona nako kukafunditsa
kwachuluka mbava nde muzikabisa
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w_ngondivuta ndi uphawi (ayi)
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w_nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w_nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 2: gwamba]
aish, conductor pokwera umati 100 ndangokhala pansi ukuti 120
aseh, osaziyamba zin_z_
muno sindichoka ngati sundipatsa change
wekha ukudziwa dollar ili pa minga
povaya kudedza pena kukwera njinga
umayesa ngati ukundiyimba
lero lonkha wandilira sindiyimva
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w_ngondivuta ndi uphawi (ayi)
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w_nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w_nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 3: gwamba]
aish, komanso yesu akufuna change mama
koma change akufuna iye si ndalama
akufunitsitsa inuyo makamaka mutasintha ndikuyamba k_mutsata
mapemphero ndi hustle ya uzimu
mukapusa tsiku lomaliza, no change
mapemphero ndi hustle ya uzimu
ukapusa tsiku lomaliza, no change
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w_ngondivuta ndi umphawi
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w_nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko change
inu ulendo w_nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
كلمات أغنية عشوائية
- dafna - i wanna feel كلمات أغنية
- joe bonamassa - is it safe to go home كلمات أغنية
- wtwice - забей (prod. wrongway!) كلمات أغنية
- m¥ss keta - condannata a danzare كلمات أغنية
- keykeh - possibilities كلمات أغنية
- shadow08 - loyalty means everything كلمات أغنية
- pullredit - зима (winter) كلمات أغنية
- negreto - miranda rights كلمات أغنية
- dylan eaton - feels like summer كلمات أغنية
- disfigured corpse - blog hyenaism كلمات أغنية