kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

emmie deebo - malire كلمات أغنية

Loading...

[intro]
that’s macia, the rhythm boy
deebo

[verse 1]
i may never be the missin’ voice
luso langa lili incomplete
ati mwaine mulibe golide i’m a mess
ati k_mwamba kulibeko malo anga
ndungotaya nthawi yanga
poti ndinaotcha kachisi ndimachimo
zatengela kulimba mtima
ndipo singachitile mwina
poti ndayenela kudza chifupi nanu, oh_oh

[chorus]
komwe ndachoka ndikutali mundilandire
zomwe ndasenza ndizambili mundilandire
poti sindingasunthe anthuwa andilembela malire
nde ndi inuyo, ndi inuyo ondiombola
ondiombola ndani? (ndi inuyo, ndi inuyo, ndi inuyo)
ondiombola ndani? (ndi inuyo, ndi inuyo, ndi inuyo)
poti sindingasunthe anthuwa andilembela malire
nde ndi inuyo, ndi inuyo ondiombola

[verse 2]
kubwela pano you’re my last hope
ndabalalika and i’m deeply so, distance
ndilibe kothawila
ndeno mtima umati njenjenje, oh
ndilibe mtendere, oh lord
ndagwada pa mawondo
nde ndifuna mundisambitse, oh
mumadzi amoyo onse
mundipulumutse, yeah_yeah
[chorus]
komwe ndachoka ndikutali mundilandire
zomwe ndasenza ndizambili mundilandire
poti sindingasunthe anthuwa andilembela malire
nde ndi inuyo, ndi inuyo ondiombola
ondiombola ndani? (ndi inuyo, ndi inuyo, ndi inuyo)
ondiombola ndani? oh (ndi inuyo, ndi inuyo, ndi inuyo)
poti sindingasunthe anthuwa andilembela malire
nde ndi inuyo, ndi inuyo ondiombola

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغنية الشائعة حالياً

Loading...