kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

eminent boiz - dosage كلمات الأغنية

Loading...

verse 1

kungodzuka mawa mami kufuna. ntakuonaaa
nkona ndimabwera kwanu kusanache utha kuona

chomwe ndimafuna mami wekha sukudziwa
koma chomwe ndimafuna mami ndekha ndimadziwa

ndimataya ntima koma iwe sunditola
kukusowa sindingathe poti nthawi sindilora

tidadyetsana chani fanzi ati imangodabwa
tima yoh tikakuyesa. tokhaso. k-mangodabwa

unaonamo. mpaka lero simmadziwa
ndilibe kalikose orso unima anandisiya

dosage yanga ndiwe sindi funa kuk-misa
ena akuti overdose mu chikondi unandimiza

chorus(hook)

iiineyooo
kukhala opanda iwe sindigathe mami

ndiwe dosage yanga

umafunika nthawi yoyenerera
without u sindimava bwino ineeee

ndiwe dossage yanga- x4

m’mawa masana madzulo ndiwe babie

verse 2

iweyo nde kanyale sinkuthira madzi or manyowa
zonse unganena ndiku mvera ngati duwa

ndilibe ntima mami ndiwe amene nakupatsa
ukatalikira ndimadanda ndekha ntangofatsa

ndi. dzafusira mbeta adzandirore kwanu komwe
nsidzaopa kamulako ngati zamlomwe

mawa masana madzulo mami umafunikiraaa
opanda iwe nditha kufa
osamwinikila

ati chikondi pa chikondi imakhala nkhani ina
nde abatiya pa iweyo amapanga nkhani ina

dosage yanga ndiwe sindi funa kuk-misa
ena akuti overdose mu chikondi unandimiza

back to hook

verse 3

ati swagg imandivuta ndinakhoza mpaka fail
kodi tizinchonchonana? kukhala samatero

amanena zambiri anthuwa ndimawamva
koma sindiwatengera amavutika muntima

ineyo opanda iwe na moyo umavuta
ndiwe w-nga w-nga lady
pamaso pa chauta

dosage yokwanira sindipanga overdose
ndikapanda kukuona ndimathakugwetsa nsozi

pamavuto pa ntendere mami
umafunikira
opanda iwe nditha kufa
osapenekera

dosage yanga ndiwe sindi funa kuk-misa
ena akuti overdose muchikondi unandimiza

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...