kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

eli njuchi - ndamva كلمات الأغنية

Loading...

[intro]
oh_ah, savage
sxvage
ooo ooo ooo (oh_oh_oh)
yeah yeah (njuchi)

[verse 1]
your actions can tell me more
you can run away but you can’t hide from me
komanso, baby i know you more
i can tell when you mean it
and when you lie to me

[pre_chorus]
your actions speak louder
pamaso ndi pakamwa
misozi wulula zonse wabisa
your actions speak louder
pamaso ndi pakamwa
misozi wulula zonse wabisa

[chorus]
okay ndamva, usandiuze apa
zamu mtima mwako ndamva
olo uzibise ndamva ndamva
okay ndamva, usandiuze apa
zamu mtima mwako ndamva
olo uzibise ndamva, ndamva
[post_chorus]
ndamva, ndamva (actions)
ndamva
ndamva, ndamva (baby your actions)
ndamva
ndamva
ndamva
ndamva, ndamva

[verse 2]
status “be my keeper” yowona ndekha
“i’ll call you back” ndimadikila call osabwera
okay ndamva, ndifumepo yapa
yanga nthawi yatha
it’s over baby

[pre_chorus]
your actions speak louder
pamaso ndi pakamwa
misozi wulula zonse wabisa
your actions (baby your actions) speak louder
pamaso ndi pakamwa
misozi wulula zonse wabisa (zonse wabisa)

[chorus]
okay ndamva, usandiuze apa
zamu mtima mwako ndamva
olo uzibise ndamva ndamva
okay ndamva (ndamva), usandiuze (ndamva)
zamu mtima mwako ndamva (ndamva)
olo uzibisе ndamva, ndamva (ndamva)
[verse 3]
ndakhala zaka zambiri
muzowawa muzokhoma awiri
when did i lose my lover?
it’s as if i marriеd a stranger
simple things didn’t really matter
ili kuti romance ija?
ili kuti attention?
wali kuti ma plan aja

[outro]
okay ndamva, ndifumepo yapa
yanga nthawi yatha
it’s over baby oh
okay ndamva, ndifumepo yapa
yanga nthawi yatha
yanga nthawi yatha

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...