kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

dirty flo - usathe mawu lyrics

Loading...

[intro]
ayo famous ndakuona
sound god, f9ine ndakuona
ha, ndatseka k_mamwa sikuti ndikudabwa
ndatseka kukamwa sikusowa choyankha
ndatseka k_mamwa sikuti ndikudabwa
ndatseka kukamwa sikusowa choyankha
chabe

[chorus]
sindingachulutse zolankhula
mawu ndi amodzi ndikadzuka
ndi mawu amodzi kunyamuka
ndimava kamodzi usathe mawu (usathe mawu)
ay, ay, usathe mawu, iwe khala phe! ndati usathe mawu
ay, ay, (yah) usathe mawu (ay) , iwe khala phe! ndati usathe mawu (dirty yea!)

[verse 1]
i cannot complain sindingathe mawu ngati bububu
i listen to myself sindithoka zamchigulugulu
life is two times two timangopeleka gratitude
ma dance ndi money moves
we go harder adzukulu (eh)
usathe mawu chete wathu yekhayo ndi god
ndipo udziwe dziko litha kusintha ndi mawu amodzi (amodzi)
ndili ku party sindikuchulutsa nkhani ndi kuchulusa ma scene (scene)
ndatseka kukamwa kukanika kuyankhula abwere awiri, awiri (awiri, awiri)
ndungoyamika (okay) , ndili ndi ma plan (ma plan)
sindukhala nawo moyo “wa nanga kutani?”
zochita ndi nyanja zonena tilibe
ndingogwira nthawi koma ankhoswe adziwe
[chorus]
sindingachulutse zolankhula
mawu ndi amodzi ndikadzuka (ndikadzuka)
ndi mawu amodzi kunyamuka (ah)
ndimava kamodzi usathe mawu (usathe mawu wo my guy)
ay, ay, usathe mawu, iwe khala phe! ndati usathe mawu
ay, ay, usathe mawu, iwe khala phe! ndati usathe mawu

[verse 2]
umangoti kungoti kungoti, kungoti chani?
tikamati season, season, ukuwona ngati ndiya ndani?
chabwino boniboni, boniboni ife tapita
nalo lusoli, lusoli, watidalitsa (straight)
usazifotokoze (no), usathe mawu (no)
zithandiza chani? (iwe) zomangoti oh
pa easy kuwupeza (kuti?) like (kuti?) moyo si uwu?
pa corner cr7 atipeza menye suii (sui)
angofikira kudabwa ndazipakulira, ndayiphula akukatenga chogwilira (oh)
akunamizira kuti ndine wowukira (oh)
ine phe ku judger kuziyimilira
ndangomenya a phyu! wayziwa? wise
ndangodula phazi ma guy si size

[chorus]
sindingachulutse zolankhula (sindinga)
mawu ndi amodzi ndikadzuka (ndikadzuka)
ndi mawu amodzi kunyamuka (yah)
ndimava kamodzi usathe mawu (usathe mawu wo my guy)
ay, ay, usathe mawu, iwe khala phe! ndati usathe mawu
ay, ay, usathe mawu, iwe khala phe! ndati usathe mawu
[outro]
usathe mawu
ukhoza kuthoka koma usathe mawu
usathe mawu
ukhoza kuthoka koma usathe mawu

Random Lyrics

Hot Lyrics

Loading...