
dirty flo - sizamwana كلمات أغنية
[intro: krazie g & dirty flo ]
(oh king geoffy)
ati iyeyo ndi f_f nine
moti wekha sukuwona?
[chorus: dirty flo]
moti wekha sukuwona?
lamulo singapose mphavu ya chikondi
usandimve mwa chipongwe koma izi sizamwana
ndikhoza ku header jibiya
tayamba kufunika ndikomaliza
usamve mwa chipongwe pakapita nthawi tizavaya
[verse 1: dirty flo]
ukamva akuyimira ndine ndakayimitsa
kukatengera shot koma she still don’t get the picture
pena kamangomva zina ndiku kamba zina
ndili mkati kakundifilira pansi pa mtima
ati ex wake ankati plain
ndati usavutike ndikupanga explain
ndisungize asamakuzunguze brain
wati bola ngati ungapange sustain
olo nsakapatse attention she can freely engage
nkofewa koma ndi chitsulo chif_kwa ndika ngenge
tinak_mana tokha tokha she don’t see nothin’ strange
[bridge: dirty flo]
nthawi ndi money ndipo yathu tikuyenera ti spend (kuti tispendе)
nthawi ndi yathu titha kuyiponya front kuti tiyithamangitse (kuti tiyithamangitse)
yeah
[chorus: dirty flo]
moti wеkha sukuwona?
lamulo singapose mphavu ya chikondi
usandimve mwa chipongwe koma izi sizamwana
ndikhoza ku header jibiya
tayamba kufunika ndikomaliza
usamve mwa chipongwe pakapita nthawi tizavaya
[outro: dirty flo]
ma baddie enake amazolowera
afuna njira yathu aziyizolowera
nde uzangowona waziona izi siza nthabwala
ha dirty
كلمات أغنية عشوائية
- zoë johnston - starlight كلمات أغنية
- iamnoclue - take back كلمات أغنية
- entheos - darkest day كلمات أغنية
- gallagher & lyle - thoughts from a station كلمات أغنية
- jason voriz - j'ai pas confiance en toi كلمات أغنية
- mischa - jane jetson كلمات أغنية
- prismala - miss interpretation كلمات أغنية
- compass hb - from the heights كلمات أغنية
- mach-hommy & tha god fahim - from vailsburg to vaudeville كلمات أغنية
- clearcurse - bad advise كلمات أغنية