crispy malawi - the weeknd كلمات الأغنية
[verse 1: crispy malawi]
pomwe pali bho_po ifeso tili pompo (ifeso tili pompo) (pompo)
koma komwe kwavaya gulu lakolo, suzatipeza konko (sungatipeze konko) (konko)
ndili pa easy sindikuyaka ndangodekha ndungosipper coco (ndungosipper coco) (coco)
koma utha ku trappa baby gin alembe bill yanga pompo (pa bill yanga pompo) (iwe) olo
olo fanta utha ku trappa f_kwa si ine malinga, ndine spe_malawi mfana wama d_nkamu
ndili nj_pa koma undipeza m’tikamu (uh huh)
zisangalalo zodanda ndazitsika
(huh, huh, huh)
sizimachitika chitika koma leroli zachitika (hee, hee, hee)
kufewa, kufewa, kufewa ine si swazi wa chipika
[chorus : crispy malawi]
weekend ndimashala stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem
take me back to the old days tikuyakakira mbowe, gazebo ndipa game
homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu
rest in peace to martse nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu
bed ndi tulo mkati ife tigona panja (lero tigona panja)
ndingofuna good vibes only, bad energy panja (bad energy panja)
girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (boys ingofuna zaza)
ma babe anu sali safe, boys yanga ili outside
[verse 2 : krazie g]
from mzuzu to the bay, mad victions and the lake[?]
pa denga and the lake, underrated, underpaid
outdated all these fakes, now it’s money over s_x
koma thako tagwedeza ndiziponya cash ineyo (later)
ndiyathu ija, kukonda chills ndine june, mpasha yama ninja
tingoplaya tima tune, yatsa zaza ija
ndili chaku moon ndi honey wachi figure, koma ndi singer, andisoka mwina (mwina)
kubwera sober pamalo tayakitsa (tayakitsa)
tili panja ndi boys ya inside (inside)
yang’anitsitsa iyi ndi street fight (fight), ndizima peace sign
monalisaaaa (yeah)
monalisaaaa (yeah)
[chorus : crispy malawi & base cube]
weekend ndimashala stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem
take me back to the old days tikuyakakira mbowe, gazebo ndipa game
homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu
rest in peace to martse nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu
bed ndi tulo mkati ife tigona panja (lero tigona panja)
ndingofuna good vibes only, bad energy panja (bad energy panja)
girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (boys ingofuna zaza)
ma babe anu sali safe, boys yanga ili (ayy) (ayy) (ayy) outside
[verse 3 :base cube]
ndi boys tikuchiller ka, ku blues tingofila ka
olimbana nafe ali m’madzi tik_mwa miller ka
spe wapota riffer ka, uku ndikusipper ka
mfana wodelera wak_mana nayo inkata
we livin’ a soft life but we go hard on these punches
i’m with the homies mahn so you know some times we get rachet and may leave you in crutches
koma tayima kaye tikuchiller ase
these ladies just want me to tap f_kwa ndiku dripper ase
ndinafika ase nde kenako ndinapita ase ndikuballer opanda keeper ase
zi bhawa tikungothila ase
spiced up ngati rajah tadya zaza ase, meek kweza speaker ase
weekend sitiyambilatu friday, utipeza thursday man tikungofila aire
sat_rday ndili pa easy ndili ndi boys tikuwupeza
mafana oyera mtima koma tik_mana pa zodetsa eish!
[chorus : crispy malawi]
weekend ndimashala stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem
take me back to the old days tikuyakakira mbowe, gazebo ndipa game
homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu
rest in peace to martse nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu
bed ndi tulo mkati ife tigona panja (lero tigona panja)
ndingofuna good vibes only, bad energy panja (bad energy panja)
girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (boys ingofuna zaza)
ma babe anu sali safe, boys yanga ili outside
[outro]
cheo meek hihihihi hihihihi
كلمات أغنية عشوائية
- nina (uk) - unnoticed كلمات الأغنية
- kristallo stone - these hands كلمات الأغنية
- the buildings - flesh and code كلمات الأغنية
- tomorrow x together - txt - 0x1=lovesong (i know i love you) - spanish ver. كلمات الأغنية
- sqpce - synap sex كلمات الأغنية
- alyson mcnamara - faithful company كلمات الأغنية
- shinigami - luv كلمات الأغنية
- greentea peng - party hard interlude كلمات الأغنية
- daniil yun - ожерелье كلمات الأغنية
- wisher (gr) - wra mhden كلمات الأغنية