kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

crispy malawi - ndi angati? كلمات أغنية

Loading...

[intro]
ndi angati omwe amafila akamvera nyimbo za spe? (ndi angati?)
(horus on the beat)
ndi angati omwe amati akamvera ndikupanga relate? (ndi angati?)
ndi angati amatikonda? ndi angati akupanga hate? (ndi angati?)
ndi angati angabwere ku show ya spe ndikupayer pa gate? (ndi angati?)

[chorus]
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)

[verse]
mhu (yeah)
ndikudziwa mulipo ambiri koma ndungofuna figure
ku checker numbers pa net eh! ndik_mabalalika
ma guy kujowela wave ya audiomack ine ndikugunda mita (mita)
ma zaza ndi juice mu cup eya sindikusipper liquor
ndine street n_gga ndikangotsika pa stage ukandipeza ku market
ma plug nde ali paliponse uzingosankha ma socket
mfana siweso ka coolest, eya usamayaluke
you just ka little kid, spe ndi ceo link ndibwana wako ntayatsa dubi
kodi ndili ndi ma ex angati? mutu mw_ngamu muli ma hater angati?
ma friends angati? satana akufuna ine nditafa
ndi angati anakuwuza spe akupenga?
ukawawuze akulenga, yeah we back in business chilichonse tikutenga
flow ya sick beat kuyipatsa matenda
[pre_chorus]
ndi angati omwe amafila akamvera nyimbo za spe? (ndi angati?)
ndi angati omwe akati akamvera ndikupanga relate? (ndi angati?)
ndi angati amatikonda? ndi angati akupanga hate? (ndi angati?)
ndi angati angabwere ku show ya spe ndikupayer pa gate? (ndi angati?)

[chorus]
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)
ndi angati? (ndi angati?)

[outro]
ndi angati? tawerenganani k_meneko
mulipo angati
eh angati?
angati?
tungofuna kudziwa man tikayamba zimavuto kusiya man
spe ndi dealer man mukamabwera mumafunika ku dhila man

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغنية الشائعة حالياً

Loading...