
crispy malawi - chibompi كلمات أغنية
[intro]
it’s nice it’s nice
mmh baby mmh come on
mmh baby
ayo landie
mmh mmh mwana salira (ay_ay, ay_ay)
mmh mmh mwana (ay_ay, ay_ay) salira (okay_okay)
ufuna chani? hmm?
[chorus]
chibhompi (uh_huh, uh_huh)
mwana akufuna chibhompi (uh_huh)
mwana akufuna chibhompi (ukufuna chani huh?)
mwana akufuna chibhompi
nditha kupatsa chimodzi, bola usayambe kudya dothi
vuto lake kukupatsa chibhompi, uyamba kundipatsa chikondi
[verse 1]
nde ana ija mafunso ngati uli court
nali busy kufotokoza zoti “mene umandiwonera muja ineyo tingatayane”
“iwe chibhompi cha ulere inuyo mungagawane hee?”
tanena “a” eh tananena “e” ah wawona?
nde uziti zandibanda ndikangoyamba kukhafa?
tiye kubafa yama lover (uh_uh_uh) (mmh_hm_mmh_hm)
[chorus]
chibhompi (mmh hm)
mwana akufuna chibhompi (ukufuna chani huh?)
mwana akufuna chibhompi
mwana akufuna chibhompi
nditha kupatsa chimodzi, bola usayambe kudya dothi
vuto lake kukupatsa chibhompi, uyamba kundipatsa chikondi
[verse 2]
ine kuyiwala zoti ndili ndi mwana man (umatani?)
kuyamba kukamba zaku kanakan[?] (zachamba eti)
boys kundithila no fireman
nangotaya man ndili ndi ma man
ati “spe usamakonde kusuta chonchi”
ndampatsa ya banana flavour yapa couch
nde mix ana amakonda ntochi kamba puff ndi chibhompi
[chorus]
hmm
chibhompi (uh_uh_uh)
mwana akufuna chibhompi (akufuna chibhompi mwanayi)
chibhompi (uh_huh)
mwana akufuna chibhompi (uh_huh uh_huh)
nditha kupatsa chimodzi (eko eko) bola usayambe kudya dothi
vuto lake kukupatsa chibhompi uyamba kundipatsa chikondi
chibhompi (uh_huh)
mwana akufuna chibhompi
‘mwana akufuna chibhompi
mwana akufuna chibhompi (tontholola)
[outro]
mwana salira
eko chibhompi
eko
we ain’t got no time
mwana wabwino
mwana wabwino
كلمات أغنية عشوائية
- boy & bear - ghost 11 كلمات أغنية
- 萧全 - 海草舞 كلمات أغنية
- simon armitage - the clown punk كلمات أغنية
- max frost - put it on me كلمات أغنية
- phil fresh - i'm the man كلمات أغنية
- lewis capaldi - hollywood كلمات أغنية
- lady of the sunshine - kings black magic كلمات أغنية
- dj khaled feat. cardi b & 21 savage - wish wish كلمات أغنية
- ted park feat. jessi - drippin كلمات أغنية
- urban cone - rocketman كلمات أغنية