
crispy malawi - angobwerabe كلمات أغنية
[intro]
f_f9ine
[pre_chorus]
ma babe ambiri man angobwerabe
43, chimaliro , nyambadwe
ena ali single ena umake
ali ndi a eniake
ali single ngati ali ku party
[chorus]
ali single ngati ali ku party
akufila ati tik_mane
sitik_mvana ngati sitingadyane
ofila dancehall sangamanyade
[verse 1]
nnamukwera kale sanganditsike
ati ali ndi guy oti sangamu cheaty
ex w_nga wina anagwidwa ndi dj
koma ntafuna nditha k_mu caller kuti ndimu_
k_mudeleter ngati amangooneka bho pa ma pictures
ama roller ndi adani k_mawauza kuti andidisse
nnangoziwa kuti si level basi k_mandipanga compare ineyo ndi achina piksy
iwe, yachina spe ndi 1 of 1 sungamafananize
sindingakunamize, ngati sufila dancehal sindingakukakamize
nditha kushala nawe koma sindingakhalitse
umuuzenso blesser wako ndikugulisa ma lipha ndi ma t shirt
osamaphwеkesa mission
[pre_chorus]
ma babe ambiri man angobwerabе
43, chimaliro , nyambadwe
ena ali single ena umake
ali ndi a eniake
ali single ngati ali ku party
[chorus]
ali single ngati ali ku party
akufila ati tik_mane
sitik_mvana ngati sitingadyane
ofila dancehall sangamanyade
كلمات أغنية عشوائية
- morris day - everlasting كلمات أغنية
- chxpo, fat panda tuan - fat sumo كلمات أغنية
- jaya the cat & the forum walters - no no song كلمات أغنية
- jesse y joy - u rock (en estudio) كلمات أغنية
- anacondaz - грязные мысли (dirty thoughts) كلمات أغنية
- loc saint - chop tonight كلمات أغنية
- get set go - sweet little kisses كلمات أغنية
- alisabeth von presley - (i'm a) wonder كلمات أغنية
- yamine - there she goes كلمات أغنية
- tata young - my world's spinning كلمات أغنية