
crispy malawi & dirty flo - wakuba (interlude) كلمات أغنية
[intro: dirty flo]
aku recorder ndi yashie
iwe aku recorder ndi yashie
iwe aku recoder ndi yashie
[pre_chorus: crispy malawi, dirty flo, both]
wakuba
amawoneka woyera koma ndi mkazi wakuda (eh)
mkazi wak_mpanda koma looks ndipanja wakunja (yea)
olo k_muloleza amatenga mwakuba
koma ali safe ali m’manja mwakuba
[chorus: dirty flo, dirty flow & crispy malawi]
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
[verse: crispy malawi & dirty flo]
k_mu caller dirty ati iyeyo ali kwa duda
kuyithoka boys yanga ati samasuta
koma amazanditenga kuvaya kwa plug koma kusonkha yamafuta
ndimadya ndine koma kungoti ghetto simakhuta
malo si ake koma ndadabwa wamasuka
attention yanga sinduyiwona ndani wasunga? (yeah)
atha kubela mpweya iwe ndikubanika
ofunika k_mu searcher uyu akamapita (mh)
(yeah, yeah) nde akamavina mpamene umaziwa kuti ass yangodzadza ndi ma fats
amangokwiya ati ndimachulutsa ma facts
pa tiktok ndimafila f_kwa ali ndi chi nyash
olo mbina ndamudabwa mene wanyamulira
waba uku koma uku nkomwe wajudukira
timuphika f_kwa watibela chopakulira
waba moto fanzi ikuwona ngati wazimitsira
[pre_chorus: crispy malawi, dirty flo, both]
wakuba
amawoneka woyera koma ndi mkazi wakuda (eh)
mkazi wak_mpanda koma looks ndipanja wakunja (yea)
olo k_muloleza amatenga mwakuba
koma ali safe ali m’manja mwakuba
[chorus: dirty flo, dirty flow & crispy malawi]
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
كلمات أغنية عشوائية
- skyzoo - collateral كلمات أغنية
- phish - birthday كلمات أغنية
- plk - freestyle "courir" كلمات أغنية
- goldbär - logan كلمات أغنية
- kevin gates - love or lust كلمات أغنية
- lil salamander - glock 17 9mm كلمات أغنية
- beyond the dream - predator's bride كلمات أغنية
- pauly g - centennial كلمات أغنية
- lil prozac - fart on you niggas كلمات أغنية
- hanging garden (us) - an urge to withdraw كلمات أغنية