kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

charisma (mw) - back to sender كلمات الأغنية

Loading...

[chorus: eli njuchi, kell kay & teddy]
phone umadzangova “h_llo, man mkazi uja lero”
zomwe apanga ndimbola
mamuna aliyense angolola
munkati mwapeza ka girl, koma mwazinamiza sikam’ngelo
koma zachimwana, zachibwana mungonamizana
back to sender
za ine ndi mkazi w_nga ayang’anila ndi ambuye
(sender, ah_yeah, ah_yeah, ah yeah)
back to sender
zomwe zikanike nzayinu ndi akwanuwo
(sender, ah_yeah, ah_yeah, ah yeah)
back to sender

[verse 1: charisma]
is it the fact that we balling?
or you heard the fact she my darling?
just because we’re shining
mpaka k_mapeka nkhani
so back to sender
mkazi w_nga siwoyendayenda
mukapitiliza nzakugendani
mutijeda breda nzosayenda
ena akathela kujahena

[refrain: charisma & kell kay]
zomwe mukupanga ndikuziwa kale
basi kubwera kufuna kunditchela ndale
cholinga mkazi w_ng_yo ndimutaye
mukunama nafe ma guy
wachitemwa w_nga iwe
true lover iwe
mkazi w_nga tisamamvere
wachikondi w_nga iwe
true lover iwe
mkazi w_nga tisamamvere
[chorus: eli njuchi, kell kay & teddy]
phone umadzangova “h_llo, man mkazi uja lero”
zomwe apanga ndimbola
mamuna aliyense angolola
munkati mwapeza ka girl, koma mwazinamiza sikam’ngelo
koma zachimwana, zachibwana mungonamizana
back to sender
za ine ndi mkazi w_nga ayang’anila ndi ambuye
(sender, ah_yeah, ah_yeah, ah yeah)
back to sender
zomwe zikanike nzayinu ndi akwanuwo
(sender, ah_yeah, ah_yeah, ah yeah)
back to sender

[verse 2: charisma]
komwe tinak_mana kunalibeko
nafusira inu kulibeko
chonde ndisiyileni nasibeko
anandipatsa ndi ambuye kuti eko
e_e_eko, so we take over
yeah, we like queen b and hova
like mr eazy, tell her leg over
she’s the only one i can’t get over

[refrain: charisma & kell kay]
zomwe mukupanga ndikuziwa kale
basi kubwera kufuna kunditchela ndale
cholinga mkazi w_ng_yo ndimutaye
mukunama nafe ma guy
wachitemwa w_nga iwe
true lover iwe
mkazi w_nga tisamamvere
wachikondi w_nga iwe
true lover iwe
mkazi w_nga tisamamvere
[chorus: eli njuchi, kell kay & teddy]
phone umadzangova “h_llo, man mkazi uja lero”
zomwe apanga ndimbola
mamuna aliyense angolola
munkati mwapeza ka girl, koma mwazinamiza sikam’ngelo
koma zachimwana, zachibwana mungonamizana
back to sender
za ine ndi mkazi w_nga ayang’anila ndi ambuye
(sender, ah_yeah, ah_yeah, ah yeah)
back to sender
zomwe zikanike nzayinu ndi akwanuwo
(sender, ah_yeah, ah_yeah, ah yeah)
back to sender

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...