kalimah.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

brainlock boi sticx - ndekha كلمات الأغنية

Loading...

[intro: boi sticx]
blxck fyxh i wanna use it as a target
ahuh!, ahuh!, ahuh!
drock on the beat
yea!
yea!
ahuh!
amatifitira mu ghetto tinawapanga hypnotize
game sili mwanja mwawo sangatiuze wise
tikadropper track yabho amapanga criticize
zanga paye audiomack k_mupanga monetize
ndisiya bwanji ngini yoti nnayamba ndekha?
tizingodroppabe kaya aziphweketsa
ndisiya bwanji ngini yoti nnayamba ndekha?
tidzingodroppabe kaya aziphweketsa

[verse 1 : boi sticx]
ili ndi luso lomwe jah anandipatsa
sindikuonaposo wina i need my flowers
muli wuli wa nyane ku katawa
zaza zomwe tiku dyazi ndizowawa
ndimapanga za ine ndekha am so creative
told my brothers to relax nzakukwezani ndege
ndika pusha dancehall amabwera ndi reggae
kufika ndichi batttle face aku signer cheque
[chorus: boi sticx]
amatifitira mu ghetto tinawapanga hypnotize
game sili mwanja mwawo sangatiuze wise
tikadropper track yabho amapanga criticize
zanga phee audiomack k_mupanga monetize
ndisiya bwanji ngini yoti nnayamba ndekha
tidzingodroppabe kaya aziphweketsa
ndisiya bwanji ngini yoti nnayamba ndekha?
tidzingodroppabe kaya aziphweketsa

[verse 2: king kryptic]
action, they all asking ’bout what happened
met my boy from the 25 and we ’bout to get into some traction
hmm subtraction
they dont really feel my caption
’cause they don’t know what happened
’cause they dont know what happened
i see two, four, six, eight shooters at the door
know that it’s the gang don’t miss the call
i see two, four, six, eight haters leave the door
’cause they know that sticx gon’ ring they phone

[outro:boi sticx]
ndisiya bwanji ngini yoti nnayamba ndekha?
tizingodroppabe kaya aziphweketsa
ndisiya bwanji ngini yoti nnayamba ndekha?
tizingodroppabe kaya aziphweketsa
drock on the beat

كلمات أغنية عشوائية

كلمات الأغاني الشهيرة

Loading...