alick macheso - kunditaya كلمات أغنية
[intro: jonas kasamba]
al!ck macheso, agitate of sungura, atomic bomba
[verse 1: al!ck macheso]
abambo anga inu, zomwe munapanga sizinthu zabwino ndithu
abambo anga inu, zomwe munapanga sizinthu zabwino ndithu
ndizabwino kwainuyo, koma kwaine sizomwe, chimodzimodzi ndi amayii
ndizabwino kwainuyo, koma kwaine sizomwe, chimodzimodzi ndi amayii w_nga oooo
[verse 2: al!ck macheso]
kunditayirira ine ngati mbuzi ine, abambo anga mulibe chisoni
kunditaya, kunditaya, kunditayira mudzenje abambo anga ine ndithu
kunditaya, kunditaya, kunditayira muchitini abambo anga ine ndithu
[verse 3: al!ck macheso]
kunditayirira ine ngati mbuzi ine, abambo anga mulibe chisoni
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
[chorus: al!ck macheso]
abambo anga ine (abambo anga ine), umoyo w_nga ine (umoyo w_nga ine), wokulira muumphawi (wokulira muumphawi), ndine mwana wa masiye ine (ndine mwana wa masiye ine)
zomvetsa chisoni, ndithu siumoyo wosangalatsaa
[outro: al!ck macheso]
ndilibe chomwe ndingapange ineyo chif_kwa ndine mwana
chimene chinakupatsani kuti mupange zimenezi
(abambo anga inee ndithu)
ndilibe chomwe ndingapange ineyo chif_kwa ndine mwana
chimene chinakupatsani kuti mupange zimenezi
كلمات أغنية عشوائية
- lil lil pp - i stubbed my toe كلمات أغنية
- jeec - ii i die tonight (acoustic version) كلمات أغنية
- nadin amizah - sorak sorai كلمات أغنية
- xclipxz - energy كلمات أغنية
- ephrem4r - uds كلمات أغنية
- iamsleepless - lonely skies كلمات أغنية
- roku145 - like this كلمات أغنية
- kari jobe feat. cody carnes - the blessing كلمات أغنية
- mc maha - preto otaku vs london gangsta كلمات أغنية
- nanda?! - notice me, senpai كلمات أغنية