
alick macheso - impfa nimulandi كلمات أغنية
[intro: jonas kasamba]
yeeeeeeh! chesology!
[chorus: al!ck macheso]
impfa nimulandi, nimulandi
inandilanda, kundilanda makolo anga
impfa nimulandi, nimulandi
inandilanda, kundilanda makolo anga amayo
[verse 1: al!ck macheso]
impfa ndikawalala, inandibera
nzanga w_nga, _n_li wachikondi
impfa ndikawalala, inandibera
nzanga w_nga, _n_li wachikondi mayo
[verse 2: al!ck macheso]
anzathu impfa nimulandi, ndithu inatilanda
kutilanda achibwenzi wathu
anzathu impfa nimulandi, ndithu inatilanda
kutilanda anzanga, achibale amayo
[verse 3: al!ck macheso]
impfa siyisankha, khuti uyu ndiwandani imangotenga chabe
impfa siyisankha, khuti uyu ndiwandani imangotenga chabe amayo
[verse 4: al!ck macheso & elton muropa]
liwa ndomoyipi, ekuelingaa, eyi_elinga, golongani nanga
liwabi khumba_khumba, eyi_elinga, eyi_elinga, golongani nanga
(al!ck)
[verse 5: al!ck macheso]
impfa nimulandi anzanga, inandilanda, inandilanda
kundilanga mwana w_nga, omwe ndinabala kundisiya nandilira amayo
anzanga impfa nimulandi, inandilanda, inandilanda
kundlianga munzanga w_nga, _n_li wachikondi
kundisiya chocho
impfa nimulandi amayo, nimulandi ndikawalala
kutilanda makolo athu, omwe anatibala, kutisiya natilira atatee
chabwino makolo athu, mupume muntendere, (k_mwamba muliko mkomwe mukonze malo athu iiyii_yii_yii oooh_aaah!)
chabwino amayi anga mupume muntendere, (k_mwamba muliko amayo mukonze malo anga iiyii_yii_yii oooh_aaah!)
[verse 6]
[?]
كلمات أغنية عشوائية
- yef omit - олух (oaf) كلمات أغنية
- faerybabyy - my life's a movie (derogatory) كلمات أغنية
- ianno - bloody angel كلمات أغنية
- felix avitia - coffee jacket كلمات أغنية
- chris allen hess - what's new, scooby-doo? كلمات أغنية
- flying squid - kafka esque كلمات أغنية
- renacimiento 74 - frescas rosas كلمات أغنية
- the mini.ster - fight كلمات أغنية
- vawex - weapon* كلمات أغنية
- sadandsolo - ps2 كلمات أغنية